MIYAMBO 13:4 — Munthu ________ amakhumbira zinthu koma sapeza kanthu, koma munthu wakhama adzalemera.
mtendere
waulesi
ulemerero
MIYAMBO 21:5 — Zolinga za munthu wakhama zimachulukitsa zinthu zake; koma aliyense wochita zinthu ________ amadzakhala wosauka.
nsalu
mwanga
mofulumira
MIYAMBO 11:27 — Iye amene amafunafuna zabwino mwakhama ________ zabwinozo, koma wofunafuna zoyipa zidzamupeza.
Amasunga
amapeza
amadana
AHEBRI 11:6 — Ndipo popanda chikhulupiriro nʼkosatheka kukondweretsa Mulungu, chifukwa aliyense amene amabwera kwa Iye ayenera kukhulupirira kuti Mulungu alipodi ndi kuti Iye amapereka ________ kwa amene akumufunitsitsa.
wosatha
chiyembekezo
mphotho
MACHITIDWE A ATUMWI 18:24 — Pa nthawi yomweyi Myuda wina dzina lake ________, mbadwa ya ku Alekisandriya anafika ku Efeso. Anali munthu wophunzira ndi wodziwa bwino Malemba.
Apolo
Akaya
Korinto
2 PETRO 3:14 — Chomwecho okondedwa, popeza inu mukudikira zimenezi, chitani changu kuti mukhale wopanda chilema kuti mukhale pa ________ ndi Iye.
mphamvu
mtendere
Ngakhale
2 PETRO 3:10 — Koma tsiku la Ambuye lidzafika ngati ________. Pa tsikuli zinthu zakumwamba zidzachoka ndi phokoso lalikulu. Zinthu zonse zidzawonongedwa ndi moto, ndipo dziko lapansi ndi zonse zili mʼmenemo zidzapsa.
2 PETRO 1:3 — Mulungu mwa ________ zake anatipatsa zonse zofunika kukhala moyo opembedza, potidziwitsa za Iyeyo amene anatiyitana ku ulemerero wake ndi ubwino wake.
chisomo
mphamvu
nyenyezi
1 PETRO 2:9 — Koma inu ndinu anthu osankhidwa ndi Mulungu, ansembe achifumu, mtundu woyera mtima, anthu ake enieni a Mulungu, munasankhidwa kuti mulalikire za ntchito zamphamvu za Iye amene anakuyitanani kuti mutuluke mu ________ ndi kulowa mʼkuwunika kwake kodabwitsa.
mdima
ulamuliro
chilungamo
AFILIPI 4:8 — ________, abale, muziyika mtima wanu pa zinthu zilizonse zabwino ndi zotamandika monga, zinthu zoona, zinthu zolemekezeka, zinthu zolungama, zinthu zoyera, zinthu zokongola ndi zinthu zosiririka.
makamaka
mwamphamvu
Potsiriza
AFILIPI 4:6 — Musade nkhawa ndi kanthu kalikonse, koma pa china chilichonse, mwa ________ ndi chidandaulo pamodzi ndi chiyamiko, perekani zopempha zanu kwa Mulungu.
manyazi
wamphesa
pemphero
AROMA 12:1 — Nʼchifukwa chake ine ndikukupemphani abale, mwa ________ cha Mulungu, kuti mupereke matupi anu monga nsembe yamoyo, yopatulika ndi yokondweretsa Mulungu. Nsembeyi ndiye kupembedza kwanu kwa uzimu.