Kodi Baibulo Limati Chiyani Za Kuleza Mtima? — Kuchiyendetsa M'moyo — Mafunso a Baibulo
Pa lemba lililonse pansipa, sankhani chimene vesiyo limaphunzitsa. Mphambu yanu idzaoneka kumapeto.
Awa ndi mayeso oyesedwa. Apambaneni kuti mupeze mfundo zopita ku Satifiketi ya Chivomerezo cha Utumiki yanu.
Miyambo 16:32 — Munthu wosapsa mtima ________ amaposa munthu wankhondo, munthu wowugwira mtima wake amaposa amene amalanda mzinda.
msanga
popanda
amayenda
Ahebri 12:1 — Tsono popeza ifenso tazunguliridwa ndi gulu lalikulu la mboni, tiyeni titaye chilichonse chimene chimatitchinga, ________ tchimo limene limatikola mosavuta, ndipo tithamange ndi khama mpikisano umene tayambawu.
makamaka
okondedwa
mwamphamvu
Ahebri 10:36 — Nʼkofunika kuti mupirire kuti pamene muchita chifuniro cha Mulungu mudzalandire zimene Iye ________.
anazindikira
mdulidwe
analonjeza
Yesaya 40:31 — koma iwo amene ________ Yehova adzalandira mphamvu zatsopano. Adzawuluka ngati chiwombankhanga; adzathamanga koma sadzalefuka, adzayenda koma sadzatopa konse.
amabweretsa
amakondwera
amakhulupirira
Chivumbulutso 2:10 — Musachite mantha ndi zimene muti musauke nazo posachedwapa. Ndithu, ________ adzayika ena a inu mʼndende pofuna kukuyesani, ndipo mudzazunzika kwa masiku khumi. Khalani okhulupirika ngakhale zitafika pa imfa, ndipo Ine ndidzakupatsani chipewa cha ulemerero wamoyo.
Satana
Pilato
Adamu
Yobu 13:15 — Ngakhale Iye andiphe, komabe ndidzamukhulupirira; ndithu, ndidzafotokoza ________ wanga pamaso pake.
mlandu
mnzake
nyimbo
1 Yohane 2:17 — Dziko lapansi likupita pamodzi ndi ________ zake, koma amene amachita chifuniro cha Mulungu amakhalapo mpaka muyaya.
kubweretsa
zilakolako
nkhunda
1 Petro 1:7 — Mayeserowa abwera nʼcholinga chakuti chikhulupiriro chanu, chimene ndi chamtengo woposa wa golide, amene amawonongeka ngakhale amayengedwa ndi moto, chitsimikizike kuti ndi chenicheni. Pamenepo ndiye mudzalandire mayamiko, ulemerero ndi ________ pamene Yesu Khristu adzaoneka.
waufumu
ulemu
zipatso
Luka 8:15 — Koma mbewu za pa nthaka yabwino zikuyimira anthu amene ali ndi mtima woona ndi wabwino, amene amamva mawu nawasunga, ndipo amalimbikira mpaka amabala ________.
zipatso
thupi
mphamvu
Ahebri 6:15 — Ndipo Abrahamu atayembekezera ________, analandira zimene anamulonjezazo.
Potsiriza
makamaka
mofatsa
← Bwererani ku phunziroli