LUKA 4:18 — “Mzimu wa Ambuye ali pa Ine; chifukwa wandidzoza kuti ndilalikire Uthenga Wabwino kwa osauka. Wandituma kuti ndilalikire kwa a ________ kuti amasulidwe ndi kwa osaona kuti apenyenso, kumasulidwa kwa osautsidwa
AHEBRI 5:14 — Koma chakudya cholimba ndi cha anthu okhwima msinkhu, amene pogwiritsa ntchito nzeru zawo, aphunzira ________ chabwino ndi choyipa.
kusiyanitsa
kupitiriza
utumiki
YESAYA 40:13 — Ndani anapereka ________ kwa Mzimu wa Yehova kapena kumuphunzitsa Iye monga phungu wake?
kumene
nthambi
malangizo
AROMA 10:2 — Popeza ndiwachitira ________ kuti ndi achangu pa zinthu za Mulungu koma osati mwachidziwitso.
ukapolo
mphatso
umboni
2 PETRO 3:18 — Koma kulani mu ________ ndi mʼchidziwitso cha Ambuye ndi Mpulumutsi wathu Yesu Khristu. Kwa Iye kukhale ulemerero tsopano mpaka muyaya. Ameni.