Awa ndi mayeso oyesedwa. Apambaneni kuti mupeze mfundo zopita ku Satifiketi ya Chivomerezo cha Utumiki yanu.
2 PETRO 1:3 — Mulungu mwa mphamvu zake anatipatsa zonse zofunika kukhala moyo opembedza, potidziwitsa za Iyeyo amene anatiyitana ku ulemerero wake ndi ________ wake.
ubwino
mdima
chiweruzo
2 PETRO 1:4 — Mwa ulemerero ndi ________ wakewo, anatipatsa malonjezo opambana kwambiri ndi a mtengowapatali. Amenewa ndi malonjezo amene amakuthandizani kulandira nawo moyo wa Mulungu, titapulumuka ku chiwonongeko chimene chili mʼdziko lapansi chifukwa cha zilakolako zoyipa.
mdima
chiweruzo
ubwino
2 PETRO 1:5 — Choncho, chitani khama kuwonjezera moyo wabwino pa ________ chanu, ndipo pa moyo wabwino muwonjezerepo nzeru.
chikhulupiriro
chisomo
ulemu
MATEYU 5:16 — Momwemonso kuwunika kwanu kuwale pamaso pa anthu kuti aone ntchito zanu zabwino ndi kulemekeza ________ anu akumwamba.
2 PETRO 1:8 — Ngati zonsezi zikhala mwa inu nʼkumachuluka, zidzakuthandizani kuti musakhale aulesi ndi osapindula ndi ________ chanu cha Ambuye athu Yesu Khristu.
chidziwitso
wankhosa
chisomo
2 PETRO 1:11 — Mudzalandiridwa bwino kwambiri mu ufumu wosatha wa Ambuye ndi ________ wathu Yesu Khristu.
Afarisi
Mpulumutsi
Akanaani
AROMA 8:29 — Pakuti amene Mulungu anawadziwiratu, anawasankhiratunso kuti akonzedwe mʼchifanizo cha Mwana wake, kuti Iye akhale Mwana ________ kubadwa mwa abale ambiri.
ukapolo
woyamba
ulemu
1 PETRO 2:9 — Koma inu ndinu anthu osankhidwa ndi Mulungu, ansembe achifumu, mtundu woyera mtima, anthu ake enieni a Mulungu, munasankhidwa kuti mulalikire za ntchito zamphamvu za Iye amene anakuyitanani kuti mutuluke mu ________ ndi kulowa mʼkuwunika kwake kodabwitsa.
mdima
ulamuliro
chilungamo
LUKA 13:24 — “Yesetsani kulowa pa ________ lopapatiza, chifukwa ndikukuwuzani kuti ambiri adzafuna kulowa koma sadzatha kutero.
mngelo
khomo
umboni
MLALIKI 4:12 — Munthu mmodzi angathe kugonjetsedwa, koma anthu awiri akhoza kudziteteza. ________ cha maulusi atatu sichidukirapo.
Mlaliki
kuchotsa
Chingwe
CHIVUMBULUTSO 19:9 — Kenaka mngelo anandiwuza kuti, “Lemba kuti, Odala amene ayitanidwa ku phwando la ukwati wa Mwana ________.” Ndipo anatinso, “Awa ndiwo mawu woona a Mulungu.”